Salimo 97:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Pakuti inu Yehova, ndinu Wam’mwambamwamba wolamulira dziko lonse lapansi.+Mwakwera pamwamba kwambiri kuposa milungu ina yonse.+
9 Pakuti inu Yehova, ndinu Wam’mwambamwamba wolamulira dziko lonse lapansi.+Mwakwera pamwamba kwambiri kuposa milungu ina yonse.+