Salimo 103:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Pakuti monga mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,+Kukoma mtima kwake kosatha nakonso ndi kwapamwamba kwa onse omuopa.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 103:11 Utumiki Komanso Moyo Wathu wa Chikhristu,8/2016, tsa. 5 Nsanja ya Olonda,8/1/2011, tsa. 13
11 Pakuti monga mmene kumwamba kulili pamwamba kwambiri kuposa dziko lapansi,+Kukoma mtima kwake kosatha nakonso ndi kwapamwamba kwa onse omuopa.+