Salimo 104:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Akasupewo amapereka madzi kwa zilombo zonse zakutchire.+Nthawi zonse mbidzi+ zimapha ludzu lawo mmenemo. Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 104:11 Galamukani!,3/8/1996, tsa. 18
11 Akasupewo amapereka madzi kwa zilombo zonse zakutchire.+Nthawi zonse mbidzi+ zimapha ludzu lawo mmenemo.