Salimo 106:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndani anganene zinthu zamphamvu zimene Yehova wachita,+Kapena ndani angamutamande mokwanira?+