Salimo 106:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Kuti ndione ubwino umene mumapereka kwa osankhidwa anu,+Kuti ndikondwere pamene mtundu wanu ukukondwera,+Ndiponso kuti ndinyadire pamodzi ndi cholowa chanu.+
5 Kuti ndione ubwino umene mumapereka kwa osankhidwa anu,+Kuti ndikondwere pamene mtundu wanu ukukondwera,+Ndiponso kuti ndinyadire pamodzi ndi cholowa chanu.+