Salimo 107:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Iwo anayendayenda m’chipululu+ mopanda kanthu.+Sanapeze njira iliyonse yopita kumzinda woti azikhalamo.+
4 Iwo anayendayenda m’chipululu+ mopanda kanthu.+Sanapeze njira iliyonse yopita kumzinda woti azikhalamo.+