Salimo 107:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Amasandutsa mitsinje kukhala chipululu,+Ndiponso akasupe a madzi kukhala malo opanda madzi.+