Salimo 108:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pokhala woyera, Mulungu walankhula kuti:+“Ndidzakondwa ndi kupereka Sekemu+ ngati gawo la cholowa.+Ndipo ndidzayezera anthu anga chigwa cha Sukoti.+
7 Pokhala woyera, Mulungu walankhula kuti:+“Ndidzakondwa ndi kupereka Sekemu+ ngati gawo la cholowa.+Ndipo ndidzayezera anthu anga chigwa cha Sukoti.+