Salimo 109:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Iye anali kuvala matemberero ngati chovala.+Matembererowo analowa mwa iye ngati madzi,+Ndiponso analowa m’mafupa ake ngati mafuta.
18 Iye anali kuvala matemberero ngati chovala.+Matembererowo analowa mwa iye ngati madzi,+Ndiponso analowa m’mafupa ake ngati mafuta.