Salimo 109:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Mawondo anga akugwedezeka chifukwa chosala kudya,+Ndawonda ndipo ndilibe mafuta alionse odzola.+