Salimo 109:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Amene akulimbana ndi ine avale manyazi,+Ndipo adziphimbe ndi manyaziwo ngati akudziphimba ndi malaya akunja odula manja.+
29 Amene akulimbana ndi ine avale manyazi,+Ndipo adziphimbe ndi manyaziwo ngati akudziphimba ndi malaya akunja odula manja.+