Salimo 112:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Sadzaopa uthenga woipa.+ נ [Nun]Mtima wake ndi wokhazikika,+ ndipo umadalira Yehova.+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 112:7 Nsanja ya Olonda,3/15/2009, ptsa. 27-28