Salimo 114:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Nanga inu mapiri, chinavuta n’chiyani kuti mudumphedumphe ngati nkhosa zamphongo?+Inunso zitunda, chinavuta n’chiyani kuti mudumphedumphe ngati ana a nkhosa?+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 114:6 Nsanja ya Olonda,11/15/1992, ptsa. 10-11
6 Nanga inu mapiri, chinavuta n’chiyani kuti mudumphedumphe ngati nkhosa zamphongo?+Inunso zitunda, chinavuta n’chiyani kuti mudumphedumphe ngati ana a nkhosa?+