Salimo 116:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Zingwe za imfa zinandizungulira+Ndipo ndinasautsika ngati kuti ndili m’Manda.+Ndinapitiriza kusautsika ndi kukhala wachisoni,+ Masalimo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 116:3 Nsanja ya Olonda,3/15/1987, tsa. 28
3 Zingwe za imfa zinandizungulira+Ndipo ndinasautsika ngati kuti ndili m’Manda.+Ndinapitiriza kusautsika ndi kukhala wachisoni,+