Salimo 118:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Nditsegulireni zipata zachilungamo,+ anthu inu.Ndidzalowamo ndipo ndidzatamanda Ya.+