Salimo 119:75 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 75 Inu Yehova, ndikudziwa bwino kuti zigamulo zanu ndi zolungama,+Ndiponso kuti mwandilanga chifukwa chakuti ndinu wokhulupirika.+
75 Inu Yehova, ndikudziwa bwino kuti zigamulo zanu ndi zolungama,+Ndiponso kuti mwandilanga chifukwa chakuti ndinu wokhulupirika.+