Salimo 119:117 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 117 Ndithandizeni kuti ndipulumutsidwe,+Ndipo ndidzamvera malangizo anu nthawi zonse.+