Salimo 119:170 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 170 Pempho langa lakuti mundichitire chifundo lifike kwa inu.+Ndipulumutseni monga mwa mawu anu.+