Salimo 132:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Chifukwa cha zimene munalonjeza Davide mtumiki wanu,+Musakane kuona nkhope ya wodzozedwa wanu.+