Salimo 138:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Ngakhale kuti Yehova ali pamwamba, amaona wodzichepetsa,+Koma wodzikuza samuyandikira.+