Miyambo 3:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pakuti Yehova ndiye amene uzidzamudalira,+ ndipo adzateteza phazi lako kuti lisakodwe.+