Miyambo 3:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Usakonze zochitira mnzako choipa,+ pamene iye akuona kuti akukhala nawe mwamtendere.+