Miyambo 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Zochita za wolungama zimabweretsa moyo.+ Zokolola za woipa zimabweretsa tchimo.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 10:16 Nsanja ya Olonda,9/15/2001, ptsa. 24-25