Miyambo 10:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Milomo ya wolungama imavomerezedwa ndi Mulungu,*+ koma pakamwa pa anthu oipa m’popotoka.+