Miyambo 11:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Munthu woipa amapeza malipiro achinyengo,+ koma wofesa chilungamo amapeza malipiro enieni.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:18 Nsanja ya Olonda,7/15/2002, tsa. 29