Miyambo 11:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Aliyense wochititsa nyumba yake kunyanyalidwa+ adzagwira mphepo,+ ndipo munthu wopusa adzakhala wantchito wa munthu wa mtima wanzeru. Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 11:29 Nsanja ya Olonda,7/15/2002, tsa. 31
29 Aliyense wochititsa nyumba yake kunyanyalidwa+ adzagwira mphepo,+ ndipo munthu wopusa adzakhala wantchito wa munthu wa mtima wanzeru.