Miyambo 12:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Njira ya munthu wopusa imakhala yolondola m’maso mwake,+ koma womvera malangizo ndi wanzeru.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 12:15 Nsanja ya Olonda,3/15/2003, tsa. 27