Miyambo 13:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Mwana amakhala wanzeru ngati akulandira malangizo* kuchokera kwa bambo ake.+ Koma amene sanamve chidzudzulo amakhala wonyoza.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 13:1 Nsanja ya Olonda,9/15/2003, ptsa. 21-22
13 Mwana amakhala wanzeru ngati akulandira malangizo* kuchokera kwa bambo ake.+ Koma amene sanamve chidzudzulo amakhala wonyoza.+