Miyambo 13:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Wokana kusunga mawu,+ wangongole adzamulanda chikole. Koma munthu amene amaopa lamulo ndiye adzalandire mphoto.+
13 Wokana kusunga mawu,+ wangongole adzamulanda chikole. Koma munthu amene amaopa lamulo ndiye adzalandire mphoto.+