Miyambo 16:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Milomo yolungama imasangalatsa mfumu yaikulu,+ ndipo mfumuyo imakonda munthu wolankhula zinthu zowongoka.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:13 Nsanja ya Olonda,5/15/2007, tsa. 20
13 Milomo yolungama imasangalatsa mfumu yaikulu,+ ndipo mfumuyo imakonda munthu wolankhula zinthu zowongoka.+