Miyambo 16:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Munthu wanzeru mumtima mwake adzatchedwa wozindikira,+ ndipo munthu wolankhula zabwino amakopa ena ndi mawu a pakamwa pake.+ Miyambo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:21 Nsanja ya Olonda,7/15/2007, ptsa. 9-10
21 Munthu wanzeru mumtima mwake adzatchedwa wozindikira,+ ndipo munthu wolankhula zabwino amakopa ena ndi mawu a pakamwa pake.+