Miyambo 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mnyozo umabwera limodzi ndi munthu woipa,+ ndipo chitonzo chimabwera limodzi ndi manyazi.+