Miyambo 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 n’cholinga chakuti ndikusonyeze kudalirika kwa mawu oona, kuti uthe kubwezera mawu oonadi kwa amene wakutuma?+
21 n’cholinga chakuti ndikusonyeze kudalirika kwa mawu oona, kuti uthe kubwezera mawu oonadi kwa amene wakutuma?+