Miyambo 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 pakuti ndi bwino kuti mfumuyo ikuuze kuti: “Bwera pamwamba pano,”+ kusiyana n’kuti ikutsitse pamaso pa munthu wolemekezeka amene wamuona ndi maso ako.+
7 pakuti ndi bwino kuti mfumuyo ikuuze kuti: “Bwera pamwamba pano,”+ kusiyana n’kuti ikutsitse pamaso pa munthu wolemekezeka amene wamuona ndi maso ako.+