Miyambo 25:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kambirana mlandu wako ndi mnzako,+ ndipo usaulule chinsinsi cha munthu wina,+