Miyambo 25:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Wovula malaya pa tsiku lozizira ali ngati vinyo wowawasa wothiridwa mu soda, ndiponso ngati woimbira nyimbo munthu wa mtima wachisoni.+
20 Wovula malaya pa tsiku lozizira ali ngati vinyo wowawasa wothiridwa mu soda, ndiponso ngati woimbira nyimbo munthu wa mtima wachisoni.+