Miyambo 25:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Kudya uchi wambiri si bwino,+ ndipo anthu akamafunafuna okha ulemerero, kodi umenewo ndi ulemererodi?+
27 Kudya uchi wambiri si bwino,+ ndipo anthu akamafunafuna okha ulemerero, kodi umenewo ndi ulemererodi?+