Miyambo 28:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mwamuna wamphamvu wosauka amene amabera mwachinyengo anthu onyozeka,+ ali ngati mvula imene imakokolola zinthu moti sipakhalanso chakudya.
3 Mwamuna wamphamvu wosauka amene amabera mwachinyengo anthu onyozeka,+ ali ngati mvula imene imakokolola zinthu moti sipakhalanso chakudya.