Miyambo 29:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Popanda kutsogozedwa ndi Mulungu, anthu amatayirira,+ koma odala ndi amene amasunga malamulo.+