Mlaliki 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Ndinaona kuti nzeru zili ndi phindu lalikulu kuposa uchitsiru+ monga mmene kuwala kulili ndi phindu lalikulu kuposa mdima.+
13 Ndinaona kuti nzeru zili ndi phindu lalikulu kuposa uchitsiru+ monga mmene kuwala kulili ndi phindu lalikulu kuposa mdima.+