Mlaliki 5:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pali chinthu chomvetsa chisoni kwambiri chimene ndaona padziko lapansi pano: Munthu kumangosunga chuma chake n’kudzapwetekedwa nacho.+
13 Pali chinthu chomvetsa chisoni kwambiri chimene ndaona padziko lapansi pano: Munthu kumangosunga chuma chake n’kudzapwetekedwa nacho.+