Nyimbo ya Solomo 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ife tikupangira zokongoletsa zoti uzivala kumutu. Zokongoletsazo zikhala zozungulira, zagolide,+ zokhala ndi mikanda yasiliva.” Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:11 Nsanja ya Olonda,11/15/1987, tsa. 24
11 Ife tikupangira zokongoletsa zoti uzivala kumutu. Zokongoletsazo zikhala zozungulira, zagolide,+ zokhala ndi mikanda yasiliva.”