Nyimbo ya Solomo 2:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Wachikondi wanga akufanana ndi mbawala+ kapena mphoyo yaing’ono. Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma* la nyumba yathu. Akuyang’ana m’mawindo,* akusuzumira pa zotchingira m’mawindo.+
9 Wachikondi wanga akufanana ndi mbawala+ kapena mphoyo yaing’ono. Taonani! Iye waima kuseri kwa khoma* la nyumba yathu. Akuyang’ana m’mawindo,* akusuzumira pa zotchingira m’mawindo.+