Nyimbo ya Solomo 2:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Pamtengo wa mkuyu,+ nkhuyu zoyambirira zapsa.+ Mpesa wachita maluwa ndipo ukununkhira. Nyamuka, bwera kuno wokondedwa wanga+ wokongola, tiye tizipita.
13 Pamtengo wa mkuyu,+ nkhuyu zoyambirira zapsa.+ Mpesa wachita maluwa ndipo ukununkhira. Nyamuka, bwera kuno wokondedwa wanga+ wokongola, tiye tizipita.