Nyimbo ya Solomo 2:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 “Anthu inu mutigwirire nkhandwe+ zing’onozing’ono zimene zikuwononga minda ya mpesa, chifukwa minda yathu ya mpesa yachita maluwa.”+ Nyimbo ya Solomo Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 2:15 Galamukani!,4/8/1994, ptsa. 24-25
15 “Anthu inu mutigwirire nkhandwe+ zing’onozing’ono zimene zikuwononga minda ya mpesa, chifukwa minda yathu ya mpesa yachita maluwa.”+