Nyimbo ya Solomo 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 “Ndikulakalaka ukanakhala ngati mlongo wanga,+ amene anayamwa mabere a mayi anga.+ Ndikanakupeza panja ndikanakupsompsona,+ ndipo anthu sakanandinyoza n’komwe.
8 “Ndikulakalaka ukanakhala ngati mlongo wanga,+ amene anayamwa mabere a mayi anga.+ Ndikanakupeza panja ndikanakupsompsona,+ ndipo anthu sakanandinyoza n’komwe.