Nyimbo ya Solomo 8:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 “Akadzakhala khoma,+ tidzam’mangira kansanja kasiliva pamwamba pake, koma akadzakhala chitseko,+ tidzam’khomerera ndi thabwa la mkungudza.”
9 “Akadzakhala khoma,+ tidzam’mangira kansanja kasiliva pamwamba pake, koma akadzakhala chitseko,+ tidzam’khomerera ndi thabwa la mkungudza.”