Yesaya 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kuyambira kuphazi mpaka kumutu palibe pabwino.+ Thupi lanu lonse lili ndi mabala ndi zilonda, ndiponso lanyukanyuka. Palibe amene wafinya zilonda zanuzo kapena kuzimanga. Palibenso amene wazifewetsa ndi mafuta.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:6 Yesaya 1, ptsa. 15-17 Nsanja ya Olonda,10/15/1987, tsa. 12
6 Kuyambira kuphazi mpaka kumutu palibe pabwino.+ Thupi lanu lonse lili ndi mabala ndi zilonda, ndiponso lanyukanyuka. Palibe amene wafinya zilonda zanuzo kapena kuzimanga. Palibenso amene wazifewetsa ndi mafuta.+