Yesaya 1:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Ndidzakubweretseraninso oweruza ngati pa chiyambi paja, ndi aphungu ngati poyamba paja.+ Pambuyo pa zimenezi mudzatchedwa Mzinda Wachilungamo ndi Mzinda Wokhulupirika.+ Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 1:26 Yesaya 1, ptsa. 33-34 Nsanja ya Olonda,7/1/1992, ptsa. 14-15
26 Ndidzakubweretseraninso oweruza ngati pa chiyambi paja, ndi aphungu ngati poyamba paja.+ Pambuyo pa zimenezi mudzatchedwa Mzinda Wachilungamo ndi Mzinda Wokhulupirika.+