Yesaya 2:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Munthu wodzikuza wochokera kufumbi adzawerama ndipo anthu odzikweza adzatsitsidwa.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+
17 Munthu wodzikuza wochokera kufumbi adzawerama ndipo anthu odzikweza adzatsitsidwa.+ Yehova yekha ndi amene adzakwezedwe pamwamba m’tsiku limenelo.+